Thursday, September 4, 2008

What in the World Is This?

NDANI ANGATHE KUTIPULUMUTSA KU IMFA NDI ZOBVUTA ZA MOYO UNO?
Dziwani kuti kumwamba ndi dziko lapansi kulibe wina woposa Ambuye wathu Yesu Khristu. Inde ambiri amadziwa kuti kunja kuno kuli timilungu tambiri tomwe timapembedzedwa mu njira zosiyana-siyana, ndipo mwa timilungu timeneti mulibe chipulumutso angakhale moyo ndi kuchiritsa, timilungu timeneti timachedwa milungu yakufa yopanda moyo (ZIWANDA) Koma mwa zonsezi kuli Mulungu weni-weni wa moyo kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu amene ali nazo mphamvu zochiritsa ndi kupulumutsa. Mateyu 28:18. Yesu akutero nawo ophunzira ache ndi tonse amene; Mphamvu zonse zapatsidwa kwa ine kumwamba ndi dziko lapansi. Tiyeni tilingarile zomwe Yesu anena motsikimizira wina ali yense pa zonse zimene apatsidwa ndi atate wa kumwamba; apa zikusonyeza kuti iye ndiye woyamba ndi wotsiriza; kulibenso wina angampose iye. Atate akonda mwana wache napereka m’manja mwache: Ndi iye amene amkhulurupirila iye ali nawo moyo wosatha, Yohane 3:35-36, Yohane 13:3.

~*~*~

What in the world is this? It is an excerpt from a Christian tract written in the Chichewa language by Headson Makazinga, who is a pastor and church-planting evangelist based in Nsanje, Malawi. Here is a partial, rough English translation of the paragraph above...

WHO CAN SAVE US FROM DEATH AND THE TROUBLES OF OUR LIVES?
Let us know that from heaven up to earth, there is no one who is above our Lord Jesus Christ. In this world there are so many kinds of gods, and many people are worshiping these kinds of gods. In these gods there is no salvation or even healing. These gods are called devils. But in all these gods, there is one above all dead gods. He is precious and exactly God. He is Jesus Christ, one who had all power and all authority from heaven to earth. Matthew 28:18: Then Jesus came to them and said, “All power and authority in heaven and earth has been given to me.” Beloved, let us believe the one who had all the power and authority -- Jesus Christ. See John 3:35-36 and John 13:3.

If you are curious about why I am putting this on my blog (which is my goal!), you can read more in this post from April 12: Out of Africa (A Letter from Headson Makazinga).

Virginia Knowles

No comments:

Post a Comment

Related Posts with Thumbnails